Pular para o conteúdo
Publicidade

Lucas 10

Chifani cha mundhu wa wachikondi wa ku Samaliya

25 Pambuyo mundhu mmojhi woyaluza thauko wadaima kuti wamuyese Yesu, wadamfunjha, "Oyaluza, nichite chiyani kuti nikhale ni umoyo wamuyaya?" 26 Yesu wadamuyangha, "Uzindikila chiyani yapo usoma mmalembo ya thauko la Musa? Uyazindikila bwanji malembo yameneyo?" 27 Mundhu yujha wadamuyangha Yesu, "Mkonde Ambuye Mnungu wako kwa mtima wako wonjhe, ni kwa umoyo wako wonjhe, ni kwa mbhavu zako zonjhe ni kwa njelu zako zonjhe ni, Umkonde njako ngati umo ujhikondela umwene." 28 Yesu wadamkambila kuti, "Wayangha bwino. Chita chimwecho kuti ukhale ni umoyo."

Veja também