39 Masa wadali ni mwali mnjake uyo wamatanidwa Maliya, mmeneyo wadakhala pafupi ni mmiyendo mwa Yesu kuvechela mayaluzo yake. 40 Nambho Masa wamachauchika ni njhito zambili. Ndiipo wadamchata Yesu ni kumkambila, "Ambuye, bwanji simuona kuti mbale wanga wanisiila nichite njhito zonjhe nekha? Mkambileni wakanithangatile."
Publicidade