Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 12

Uyo wafunika kuopedwa

4 "Nikukambilani anyiimwe achabwenji langa, msadawaopa anyiyawo akupha thupi, anyiyawo pambuyo pa yameneyo saakhoza kuchita chilichonjhe. 5 Nambho, sinikulangizeni uyo mufunika kumuopa, muopeni yujha pambuyo pakupha thupi wakhoza kukuponyani kumoto wosathima muyaya. Zenedi nikukambilani, muopeni iye.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também