6 Bwanji, njhwala zisano sizigulichidwa kwa mtengo waung’ono kupunda? Nambho, pamaso pa Mnungu siiwalika ata njhwala imojhi. 7 Zenedi, ata machichi ya mmitu yanu, yawelengedwa. Chipano, msadaopa, anyiimwe nde muli ni phindu kupunda kupitilila njhwala!"