11 Mnyumba mmenemo mudali wamkazi mmojhi uyo wamalamulidwa nichiwanda pavyaka khumi ni nane. Nayo wadali nichipindi, nisiwamakhoze kuima. 12 Yesu yapowadamwona wamakazi mmeneyo, wadamtana, ni wadamkambila, "Wamkazi, wamasulidwa chipindi chako." 13 Yesu yapo wadamwikila manja pamwamba pa mutu wake kwa kughafya, ghafula thupi lake lidakhululukanjho, wadayamba kumtamanda Mnungu.