Chifani cha mbeu yaying’ono ya mtengo uwo utanidwa haladali
18 Ndiipo Yesu wadafunjha, "Ufumu wa kumwamba ulingana ni chiyani? Siniulinganiche nichiyani? 19 Uli ngati mbeu yaing’ono ya mtengo uwo utanidwa haladali iyo wadaivyala mundhu mmojhi mumunda mwake. Idamela ni kukula ni kukhala mtengo waukulu, ni mbalame za kumlengalenga zidamanga visa vao mndhawi zake."