Pular para o conteúdo
Publicidade

Lucas 14

26 "Ngati mundhu waliyonjhe wafuna kukhala woyaluzidwa wanga, ifunika wanikonde ine kupitilila umo waakondela atate wake na amake, mkazake ni wana, achakulu wake ni achalongo wake, ata kupitilila umo wajhikondela mwene wake. Ngati siwachita chimwecho, siwangakhoze kukhala woyaluzidwa wanga. 27 Mundhu waliyonjhe uyo siwavemela kuvutika ni kumwalila yapo wanichata, siwakhoza kukhala woyaluzidwa wanga.

Veja também