Chifani cha Mfalisayo ni wolandila malipilo
9 Ndiipo Yesu wadakambila kwa chifani, wandhu anyiwajha amajhiona kuti avomelezeka pamaso pa Mnungu ni kwadelela wina, wadakamba, 14 Nikukambilani yujha wolandila malipilo wadabwelela kukhomo kwake wavomelezedwa pamaso pa Mnungu, kupitilila yujha Mfalisayo. Pakuti, waliyonjhe uyo wajhikweza siwachichidwe, ni waliyonjhe uyo wajichicha siwakwezedwe."