Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 19

2 Padali ni mundhu mmojhi mmujhi mmenemo wamatanidwa Zakayo. Mmeneyo wadali wamkulu wa wandhu wolandila malipilo ni wadali ni chuma chambili. 3 Iye wamafuna wamuone Yesu kuti ni mundhu wamtundu wanji, nambho wadalepela kumuona ndande iye wadali wamfupi, ni wandhu adachuluka. 4 Chimwecho, wadathamangila mchogolo, wadakwela mumtengo wa mkuyu kuti wakhoze kumuona Yesu, pakuti wamajhiwa Yesu wamapita mnjila imeneyo. 5 Yesu yapo wadafika pamalo yameneyo, wadapenya mmwamba mwa mtengo ni kumkambila, "Zakayo, chika chisanga, pakuti lelo sinikhale mlendo kukhomo lako." 6 Zakayo wadachika chisanga ni kumlandila Yesu kwa kukondwela. 7 Wandhu wonjhe yapo adaona yameneyo adayamba kudandaula ni kukamba, "Wapita kukhala mlendo wa mundhu wa machimo."

8 Nambho Zakayo wadaima ni kwaakambila Ambuye, "Vechelani Ambuye! Ine sinaninghe wosauka chuma changa chakumojhi, ningati namlanda mundhu chindhu chalichonjhe, sinimbwezele kanayi."

Veja também