61 Ambuye naonjho adang’anamuka ni kumpenyecha Petulo. Ndiipo Petulo wadakumbukila mawu yajha wadakambilidwa ni Ambuye, "Lelo siunikane katatu tambala wakali osalile." 62 Iye wadatuluka kubwalo uku ni wapwetekedwa mumtima ni kuyamba kulila kupunda.