Pular para o conteúdo
Publicidade

Lucas 3

Kubatizidwa kwa Yesu

21 Yapo wandhu wonjhe adali kubatizidwa, Yesu nayonjho wadabatizidwa. Ni yapo wadali kupembhela, kumwamba kudachekuka. 22 Ndiipo Mzimu Woyela uwo umaoneka ngati nghunda udamchikila. Ni mvekelo kuchokela kumwamba udaveka, "Iwe nde mwana wanga uyo nikukonda, nakondelechedwa ni iwe."

Veja também