Chifani cha matengo
24 Yesu wadaakambila wandhu chifani china, "Ufumu wa kumwamba ulingana ni mundhu uyo wadavyala mbeu zabwino mmunda mwake. 25 Nambho wandhu yapo adagona, mdani wake wadajha, wadavyala matengo pakati pa mapila, nikuchoka. 26 Mapila yapo yadamela ni kuyamba kubala, matengo nayo yadayamba kusetela. 27 Opota njhito adamchata mwene munda, adamkambila, ‘Imwe waakulu, simdavyala mbeu zabwino mmunda mwanu? Chipano matengo yachokela kuti?’ 28 Iye wadayangha, ‘Mdani ndeuyo wachita chimwecho.’ Ndiipo opota njhito wake adamfunjha, ‘Bwanji, ufuna tikayazule?’ 29 Iye wadaayangha, ‘Notho, msadayazula, pakuti pozula matengo, mkhoza kuzulanjho ni mapila. 30 Zisiyeni zonjhe zikulile pamojhi mbaka ndhawi yokolola. Ndhawi imeneyo sinaakambile wokolola kukusa matengo akayamange machakatamachakata ni kuyabucha. Nambho mapila kololani mkaiike mnghokwe mwanga.’"