Chifani cha khokha
47 "Chimchijha, ufumu wa kumwamba ulingana ni khokha ilo liponyedwa mnyanja ni kuvuwa njhomba za mitundu yosiyanasiyani. 48 Khoka yapo lidajhala njhomba zambili, alovi adakokela khokha kumtunda, adakhala panjhi ni kusanghula njhomba, zabwino aziika mngwangu, nambho njhomba zoyipa adazitaya. 49 Kumathelo kwa jhiko sikukhalile chimwechi, atumiki aku mwamba Amnungu siajhe nikwaapatula wandhu oyipa pakati pa wandhu abwino, 50 ni wandhu oyipa saponyedwe kumoto woofya wa muyaya, uko sikukhale kulila ni kukukuta mano."