15 Yesu wadaafunjha, "Bwanji, ni anyiimwe mkamba kuti ine ni yani?"
16 Simoni uyo watanidwa Petulo wadayangha, "Iwe nde Kilisito muomboli, Mwana wa Mnungu wali wamoyo."
17 Yesu wadayangha, "Wapachidwa mwawi iwe Simoni mwana wa Yona, pakuti ichi wachikamba siudavunukulilidwe ni mundhu, nambho Atate wanga a kumwamba.