Mbale wako yapo wachita machimo
15 "Ngati mbale wako wakalakwila, mchate umkambile kulakwa kwake muli awilipe. Wakakuvela siikhale wampata mbale wako. 16 Nambho ngati siwakane kukuvela, funa mundhu mwina mmojhi kapina awili pamojhi ni iwe, kuti mau lililonjhe lichimikizike kwa amboni awili kapina atatu ili mavuto yathele, ngati umo yalembedwa mmalembo.