12 Kuli vindhu vambili ivo vaachita waachimuna asadakwata. Wina abadwa chimwecho, ni wina achitidwa chimwecho ni wandhu kuti siadakhala ni mbhavu zachimuna. Wina saakwata ndande ya Ufumu wa Mnungu. Mundhu uyo wakhoza kuyalandila mau yaya, wayalandile."
Publicidade