Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 21

Yesu wauleswa mkuyu

18 Umawamawa yesu yapo wamabwela kuchokela ku Besaniya kupita kumujhi, wadavela njala. 19 Wadauona mtengo wa mkuyu mbhepete mwanjila, wadaupitila nambho siwadapate chipacho chilichonjhe, udali ni machambape, wadaukambila ujha mtengo, "Usadapachanjho vipacho!" Pampajha mkuyu ujha udauma.

20 Oyaluzidwa wake yapo adapenya chindhu chijha chidachitika, adadabwa kupunda ni kufunjha, "Ndande yanji mtengo uwu wauma kankamojhi?"

21 Yesu wadakambila, "Zene nikukambilani, ngati simukhulupilile popande kukayikila, mkhoza kuchita osati ichipe nachita pamtengo, nambho mkhoza kulikambila pili ili, Zuka ukajhitaye mnyanja,siikhale chimwecho. 22 Mukakulupilila chindhu chilichonjhe simpembhe mmapembhelo, simulandile."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também