Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 24

21 Pakuti nyengo imeneyo sikukhale ni mavuto yayakulu, yayo siyadachokelepo kuyambila jhiko yapo lidaumbidwa mbaka lelo, ni siyachokelanjho mavuto yameneyo. 22 Mnungu wadakayachepecha masiku yameneyo ya mavuto, ngati Amnungu wadakasiya kuzichepecha siku zimenezo, palibe uyo wadakakhoza kuomboka. Nambho ndande ya wandhu wake wasangha, Mungu wazichepecha siku zimenezo."

Veja também