Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 26

38 Kumeneko wadaakambila, "Nili ni chisoni chachikulu mumtima mwanga icho chikhoza kunipha. Khalani pano ni muchezele pamojhi ni ine."

39 Wadapita pachogolo pang’ono, wadagwa panjhi chifufumimba ni kupembhela, "Atate wanga, ngati ikhozeka, nichocheleni chikho ichi cha mavuto! Chipano osati ngati umo nifunila ine, nambho ngati umo mufunila imwe."

Veja também