Yuda wajhimangila
3 Yuda, uyo wadamng’anamuka Yesu, yapo wadaona kuti Yesu walamlidwa kuphedwa, wadandaula ni wadabweza vijha vibandhu selasini va madini ivo vitanidwa ndalama izo wadatenga kwa achogoleli a ajhukulu ni akulu a wandhu. 4 Wadaakambila, "Nalwakwa, pakuti namng’anamuka mundhu wosalakwa kuti waphedwe!"
Anyiiwo adamuyangha, "Ife tilibemo, zako umwene!"
5 Yuda wadazitaya ndalama zimenezo mnyumba ya Mnungu, ndiipo wadachoka ni kupita kujhimangila chingwe mkhosi.