25 "Ndendande nikukambilani msadajhichaucha pa umoyo wanu kuti simudye chiyani kapina simumwe chiyani kuti mkhale amoyo kapina mathupi yanu simuvale chiyani. Bwanji umoyo osati wa phindu kupitilila chakudya? Bwanji, thupi lilibe phindu kupitilila vivalo? 26 Zipenyeni mbalami, sizivyala ni sizikolola ni alibe nghokwe yaliyonjhe. Nambho, Atate wanu akumwamba azidyecha. Bwanji, anyiimwe opande aphindu kupitilila mbalami? 27 Yani pakati panu wakajhichaucha wakhoza kujhichuluchila ata saa limojhi la umoyo wake?"
28 "Ndande yanji anyiimwe mjhichauchila vivalo? Yapenyeni maduwa ya mthengo umo yakulila. Siyachita njhito kapina kujhipotela viwalo. 29 Nikukambilani, ata Solomoni mwenewake pa chuma chake chonjhe, siwadavekedwepo bwino ngati limojhi la maduwa yaya. 30 Ngati, Mnungu wayaveka chimwecho machamba ya kuthengo yayo lelo yalipo ni mawa yathilidwa pamoto, bwanji, Mnungu siwakuvekani kupunda anyiimwe? Anyiimwe achikhulupi chochepa!"
31 "Chimwecho, msadajhichaucha nimkamba, ‘Sitidye chiyani! Kapina sitimwe chiyani! Kapina sitivale chiyani!’ 32 Pakuti yameneyo yonjhe wandhu yao siamjhiwa Mnungu ajhichauchila yaya yonjhe. Atate wanu akumwamba ajhiwa kuti mfuna ivi vonjhe. 33 Chimwecho, ufuneni uti ufumu wa Mnungu ni kuchita yayo wayafuna Mnungu, ni iye siwakupacheni yaya yonjhe. 34 Ndiipo, msadajhichauchila ya mawa, pakuti mawa siijhichauchile yeneyake. Kila siku lijhichauchila lene lake."