Khomo lowonda
13 "Lowani kupitila khomo lowonda. Pakuti khomo ilo lichogoza kumalo kwa wandhu akufa ni lopanuka, ni wandhu alowela khomo limenelo ni ambili. 14 Nambho khomo ilo lichogoza ku umoyo ni laling’ono ni lowonda wandhu wochepa ndeyawo akhoza kuiona njila imeneyo."