Mwali wa wamkulu ni wamkazi mmojhi alamichidwa
18 Yesu yapo wamakamba yameneyo, wamkulu mmojhi wa Ayahudi wadamgwadila, ni kukamba, "Mwana wanga wa mwalilila chipano yapa. Nambho, nikupembha ujhe ni umsanjike manja, nayo siwakhale wamoyo."
19 Yesu wadachoka pamojhi ni oyaluzidwa wake, adachatana ni yujha wamkulu.