Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 9

2 Kumeneko adampelekela mundhu ovuwala uyo wadagona pachitala. Yesu yapo wadaona chikulupi chao, wadamkambila mundhu yujha ovulala, "Limba mtima mwana wanga! Walekeledwa machimo yako!"

3 Akumojhi awoyaluza mathauko amakambilana achinawene, "Mundhu uyu wamchita chipongwe Mnungu!"

4 Yesu wadajhiwa ivo amakambilana, wadafunjha, "Bwanji, ndande yanji mkambilana voipa? 5 Liti lili lopepuka, kukamba, Walekeleledwa machimo yako,kapina kukamba, Ima uyende?6 Chipano nifuna mjhiwe kuti Mwana wa Mundhu wali nilamulo mujhiko lakulekelela machimo ya wandhu." Pamwepo wadamkambila yujha mundhu ovulala, "Ima, tenga chitala chako, ujhipita kukhomo kwako!"

7 Pampajha Yujha mundhu wadavula wadaima ni kupita kukhomo lake.

Veja também