Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 9

Yesu wamlamicha uyo siwakhoza kukamba

32 Wandhu yapo amabwela kwao, wandhu wina adampelekela Yesu mundhu uyo simakhoze kukamba ndande wadali ni chiwanda. 33 Pampajha chiwanda yapo chidachochedwa, mundhu yujha siwamakhoze kukamba wadayamba kukamba. Wandhu adadabwa ni kukamba, "Sichidaonekepo chindhu ngati ichi sichidachokelepo mujhiko la Izilaeli."

Veja também