9 Ine nikukondani anyiimwe ngati umo Atate adanikondela ine. Khalani muchikondi changa. 10 Mkachita ngati umo afunila Atate ni kukhala muchikondi changa, ngati ine umo nichitila umo afunila Atate wanga ni kukhala mu chikondi chao."