Pular para o conteúdo
Publicidade

João 4

46 Chimwecho Yesu wadafikanjho mbaka Kukana ya ku Galilaya, kujha wadang’anamula majhi kukhala divai. Kudalipo mchogoleli mmojhi uyo wadali ni mnyamata wake uyo wamadwala kujha ku Kapelinaumu. 47 Chimwecho mchogoleli yujha yapo wadavela kuti Yesu wafika ku Galilaya kuchokela ku Yudea, wadamchota ni kumpembha wakamlamiche mwana wake uyo wamadwala pafupi kumwalila. 48 Yesu wadamkambila, "Ukalepela kuona vizindikilo ni vodabwicha siukhulupilila."

49 Mchogoleli mmeneyo wadamkambila, "Waakulu, pepani tiyeni mwana wanga wakali osafe."

50 Ndiipo Yesu wadamkambila, "Mapita pe, mwana wako walama."

Yujha mundhu wadakhulupilila mawu ya Yesu ni kupita. 51 Yapo wadali mnjila wadapezana ni mbowa zake, zidamkambila, "Mwanawako walama!"

52 Chimwecho wadafunjha ndhawi iyo mwana wadalama, adamkambila kuti, "Jhulo ndhawi ya saa saba za usana, nde yapo wadalama." 53 Ndiipo atate wake mwanayo adakumbukila kuti, ndhawi idali ijha Yesu wadamkambila, "Mwana wako walama." Ndiipo iye ni achabale wake onjhe apakhomo lake adakhulupilila.

54 Ichi chidali chizindikilo chakawili icho wadachichita Yesu, yapo wamachoka ku Yudea kupita ku Galilaya.

Veja também