Pular para o conteúdo
Publicidade

Yohana 6

48 Ine nde chakudya cha umoyo. 49 Azee wanu adadya chakudya icho chitanidwa mana ku phululu, nambho adamwalila. 50 Nambho chino nde chakudya icho chichoka kumwamba, kuti waliyonjhe uyo wakudya siwadamwalila. 51 Ine nde chakudya chili cha moyo icho chachika kuchoka kumwamba. Mundhu waliyonjhe uyo siwadye chakudya ichi siwakhale moyo muyaya. Ni chakudya icho sinimpache, nde thupi langa ilo nichocha ndande ya wandhu ajhiko la panjhi."

Veja também