Kubadwa kwa Yesu kuuzilidwa
26 Mumwezi wa sita wa pathupi pa Elizabeti, Mnungu wadamtuma mtumiki wake Gabilieli kupita kumujhi wa Galilaya, uwo utanidwa Nazaleti, 27 wapite kwa mwalimbeta uyo wamatanidwa Maliya, uyo wadapachidwa chilipa ni wammuna uyo wamatanidwa Yusufu, wa mbadwa wa Daudi.