4 Kapina anyiwajha khumi ni nane adaphedwa yapo lidagwela phupha kujha ku Siloamu, mganiza anyiiwo adali amachimo kupitilila wandhu onjhe amakhala ku Yelusalemu? 5 Nikukambilani osati nchimwecho, nambho namwenjho ngati simulapa, simuyomwe ngati anyiiwo."
Publicidade