48 Wobala wake yapo adamuona adazizwa kupunda. Maliya, make wamwanayo wadamfunjha, "Mwana wanga, ndande yanji watichitila chimwechi? Atate wako ni ine timakufunafuna tali ni mandha."