48 Wobala wake yapo adamuona adazizwa kupunda. Maliya, make wamwanayo wadamfunjha, "Mwana wanga, ndande yanji watichitila chimwechi? Atate wako ni ine timakufunafuna tali ni mandha." 49 Iye wadaafunjha, "Ndande yanji mnifunafuna ine? Bwanji, simujhiwa kuti ine nifunika kukhalapo panyumba ya atate wanga?" 50 Nambho wobala wake siadajhiwe mate ya mawu yayo wadakambila mwana wao.
51 Ndiipo Yesu wadabwela pamojhi ni anyiiwo mbaka ku Nazaleti, iye wamavela. Nambho amake adavisunga vindhu vonjhe mumtima.