Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 2

Atumiki akumwamba a Mnungu waatulukila Owesa

8 Ni pamalo pamenepo padali ni owesa amakhala pafupi ni pamenepo amalonda mbelele zao ndhawi ya usiku. 9 Mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadatulukila mwachizulumukila, ni dangalila la ulemelelo wa Ambuye lidawalila njhonga zonjhe. Nianyiiwo adaopa kupunda. 10 Nambho mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadaakambila, "Msadaopa! Nakupelekelani uthenga wabwino uwo siwakondweleche kupunda wandhu wonjhe.

Veja também