8 Ngati mujha mtengo wa vipacho ufunika kubala, nianyiimwe mlangize kwa vichito kuti mwasiya machimo yanu. Osati muyambe kujhikambila mmitima mwanu kuti, ‘Tilinawo ambuyathu Ibilahimu.’ Nikukambilani kuti Mnungu wakhoza kuichita miyala iyi kukhala mbadwa wa Ibulahimu.