18 Simupelekedwe kwa alamuli ni afumu ndande ya ine, dala mwaalalikile Uthenga Wabwino kwa anyiiwo ni kwa wandhu yao osati Ayahudi. 19 Yapo sakupelekeni kubwalo la milandu, msadakhala ni mandha kuti simukambe chiyani, pakuti simupachidwe chokamba ndhawi imeneyo.
Publicidade