15 Ujhulo yapo udafika, oyaluzidwa wake adamchata ni kumkambila, "Malo yano ni paphululu, jhuwa litobila. Walole wandhu apite kumijhi akajhigulile chakudya."
16 Yesu wadaakambila, "Siifunika achoke, anyiimwe mwachinawene wake mwaapache chakudya."
17 Anyiiwo adamuyangha, "Tulinayo mabumunda isanope ni njhomba ziwili."
18 Yesu wadaakambila, "Nipelekeleni pano." 19 Wadaakambila wandhu akhale mmaujhu. Yesu wadatenga mabumunda yasano ni njhombha ziwili zijha, wadakweza maso yake kumwamba, wadamyamika Mnungu. Halafu wadabandhula mabumunda ni kwaapacha oyaluzidwa wake, naonjho oyaluzidwa wake wadaagawila wandhu. 20 Wandhu wonjhe adadya ni kukhuta. Oyaluzidwa adakokola vidufya ivo vidakhalila ni kujhaza miseche khumi ni iwili. 21 Wachimuna yawo adadya adali ngati elufu zisano, nambho waachikazi ni wana siadawelengedwe.