18 Nambho chindhu icho chituluka mkamwa chichoka mumtima, chimenecho nde icho chimchita mundhu siwadavomelezeka pakumlambila Mnungu. 19 Pakuti mumtima yachoka maganizo ya kupha, chigololo, uhule, unami, kuba, umboni wanthila ni matukwano.