Amila ya Afalisayo ni Asadukayo
5 Oyaluzidwa wake yapo adayomboka kuchijya la nyanja, adazindikila kuti aiwala kutenga mabumunda. 6 Yesu wadaakambila, "Khalani maso ni mjhipenyelele ni amila ya Afalisayo ni Asadukayo."
7 Ndiipo oyaluzidwa adayamba kukambilana achinawene kwa achinawene, "Wakamba chimwechi ndande sitidatenge mabumunda."
8 Yesu wadayajhiwa yayo amachuchana, wadaakambila, "Imwe, wandhu mukhulupilila pang’ono! Bwanji muchuchana mwachinawene ndande yosatenga mabumunda? 9 Bwanji, mkalipe osajhiwe? Bwanji, simukumbukila mabunda yasano yajha nidapacha wandhu elufu zisano? Bwanji, mdajhaza miseche ingati ya vijha vokhalila? 10 Kapina mabumunda saba yajha mudagaawila wandhu elufu zinayi, chiwelengelo cha miseche ingati mudakusa? 11 Bwanji, simudajhiwa kuti sinimakambe nghani za mabumunda? Jhipenyeleleni ni amila ya Afalisayo ni Asadukayo."
12 Pamenepo oyaluzidwa wake adajhiwa kuti siwadakambile ajhipenyelele ndande ya amila ya mabumunda, nambho ajhipenyelele ni mayaluzo ya Afalisayo ni Asadukayo.