Kuchocha nsongho mnyumba ya Mnungu
24 Yesu ni oyaluzidwa wake yapo adafika ku Kapelinaumu, wandhu alandila nsongho wa mnyumba ya Mnungu adamchata Petulo ni kumfunjha, "Bwanji, oyaluza wanu wachocha nsongho wa mnyumba ya Mnungu?"
25 Petulo wadayangha, "Yetu, wachocha."
Petulo yapo wadalowa mkati, Yesu wadayamba kumfunjha, "Simoni, iwe uona bwanji? Mafumu ajhiko alandila malipilo ni nsongho kuchoka kwa ayani? Kwa wandhu wao kapina kuchokela kwa alendo?"
26 Petulo wadamuyangha Yesu, "Kuchoka kwa alendo."
Yesu wadamkambila, "Ni bwino, wandhu wao saafunika kuchocha nsongho. 27 Nambho sitifuna kwaakwiicha wandhu anyiyawa, pita kunyanja ukawejhe, utenge njhomba yoyamba kukodwa, uiyasamiche kamwa lake, ni mkati mwake siukomane ndalama. Itenge ukalipile nsongho yaine ni ukajhilipile iwe."