Yesu walowa ku Yelusalemu kolulutilidwa
1 Yesu ni oyaluzidwa wake yapo adawandikila ku Yelusalemu ni kufika kuchijhijhi cha Besifage, ku phili la Mizeituni, wadaatuma oyaluzidwa wake awili amchogholele, 2 wadaakambila, "Pitani mbaka chijhijhi icho chili mchogolo mwanu, simumpheze phunda wamangidwa pamojhi ni mwana wake. Amasuleni ni mnipelekele pano. 3 Mundhu wakakufunjhani chalichonjhe, mkambileni Ambuye amfuna, nayo siwakuloleni mchoke nawo."
4 Vindhu ivi vidachitika kuti yakwanile yajha kambidwa ni mlosi, niwakamba,
5 "Mkambileni mwali wa Sayuni,
‘Penya, mfumu wako watokujhela!
Mpole ni wakwela pamsana pa phunda,
mwana wa phunda.’ "
6 Chimwecho oyaluzidwa wake adapita kuchita ngati mujha Yesu wadakambila. 7 Adampeleka yujha phunda pamojhi ni mwana wake, adayala njhalu pamsana pa mwanaphunda ni Yesu wadakhala pamwamba pake. 8 Gulu lalikulu la wandhu lidayala njhalu zao mnjila ni wandhu wina adadula ndhawi zazing’onozing’ono za mitengo ni kuziyala mnjila. 9 Gulu la wandhu lidachogolela ni lijha limamchata mbuyo lidakweza mvekelo nilikamba, "Watamandidwe Mwana wa Daudi! Wamwawi yujha wakujha kwa jhina la Ambuye! Matamando kwa Mnungu kumwamba!"
10 Yesu yapo wamalowa kumujhi wa Yelusalemu, gulu lonjhe lidadabwa ni kufunjhana, "Uyu ni yani?"
11 Lijha Gulu la wandhu lidayangha, "Uyu nde Yesu mlosi wa Mnungu, wachokela kumujhi wa Nazaleti mmujhi mwa Galilaya,"