Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 25

Chifani cha anamwali khumi

1 "Ndhawi imeneyo, ufumu wakumwamba siulingane ni anamwali kumi atenga nyali zao nikupita kumlandila okwata. 2 Anamwali asano pakati pao adali asabobwa ni asano adali ni njelu. 3 Anamwali asabobwa wajha adatenga nyali zao nambho sadatenga mafuta ina, 4 Nambho anyiwaja adali ninjelu adatenga mabotolo yayo yadajhala mafuta ni pamojhi nyali zao. 5 Okwata wadachedwa kujha ni anamwali wonjhe adaojhela ni kugona.

6 "Usiku pakati padaveka mundhu niwaluluta ndhungululu, lyaa, lyaa! Mwene ukwati uyuyapa, tieni timlandile iye.7 Ndiipo anamwali wonjhe adauka ni kuzikonja nyali zao dala zikwelele bwino. 8 Anamwali asabobwa wajha adaakambila anamwali anjelu, Tigawileni mafuta yanu pang’ono, nyali zathu zitothima.9 Anamwali a njelu wajha adaayangha, Notho, siyatikwana kupungulana ife ni anyiimwe. Mbasa mpite kwa wandhu yawo agulicha mafuta mkagule yanu.10 Yapo amapita kugula mafuta, kumbuyo kwao okwata wadafika, anamwali anjelu wajha adajhikonjekela adalowa pamojhi ni okwata kuphwando la ukwati ni chicheko chidachekedwa."

11 "Pambuyo pang’ono, adajha anamwali asabobwa wajha, adatana, Imwe wakulu, imwe wakulu! Tichakulileni chicheko!12 Nambho wokwata yujha wadayangha kuti siwajhiwa ata pang’ono."

13 Ndiipo Yesu wadamalizila kukamba, "Mjhipenyelele pakuti simujhiwa siku kapina saa."

Veja também