19 Waliyonjhe uyo siwachata thauko laling’ono kuchokela mthauko ili nikwaayaluza wina kuti achite chimwecho. Mmeneyo siwakhale womng’ono kupunda mu ufumu wa kumwamba. Nambho yujha wachata thauko ni kwaayaluza wina, mmeneyo siwakhale wamkulu mu ufumu wa kumwamba.