Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 5

19 Waliyonjhe uyo siwachata thauko laling’ono kuchokela mthauko ili nikwaayaluza wina kuti achite chimwecho. Mmeneyo siwakhale womng’ono kupunda mu ufumu wa kumwamba. Nambho yujha wachata thauko ni kwaayaluza wina, mmeneyo siwakhale wamkulu mu ufumu wa kumwamba. 20 Zene nikukambilani ngati simuchita umo wafunila Mnungu kupitilila umo achitila Afalisayo ni oyaluza a thauko simulowa mu ufumu wa kumwamba ata pang’ono."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também