Kubadwa kwa Yohana m’batizi kuuzidwa
5 Pa ndhawi ya Helode mfumu wa Kuyudea, kudali mjhukulu wa Mnungu mmojhi uyo wamatanidwa Zakaliya, wochokela kugulu la anjhembe la Abiya. Nayonjho Elizabeti, mkazake Zakaliya wamachokela kukhamu la wanjhembe la Aloni. 6 Zakaliya ni mkazake Elizabeti adali wandhu yawo wovemelezeka pamaso pa Mnungu. Amakhala kochata malamulo ni thauko la Mnungu.