Chifani cha phwando lalikulu
15 Ndiipo yapo wadavela yameneyo, mundhu mmojhi pakati pa wandhu wajha adakhala ni Yesu wadamuyangha, "Wali ni mwawi mundhu uyo siwadye chakudya cha phwando la Ufumu wa Mnungu!"
24 Pakuti nikukambilani, palibe ata mmojhi wa wandhu wajha alalikidwa ni kukana, uyo siwalowe ni kudya chakudya changa paphwando.’ "