20 Ndiipo wadayamba ulendo wopita kwa atate wake. Nambho yapo wadali wakali patali, atate wake adamuona, adamlengela lisungu. Adamthamangila mwana wao ni kumkhumbatila kwa chisangalalo.