19 Ndiipo, wadatenga bumunda, wadayamika, ni kuubandhula, wadapacha atumwi ni kukamba, "Ili ni thupi langa ilo lichochedwa ndande ya anyiimwe. Mjichite chimwechi ponikumbukila ine." 20 Chimwecho, yapo adamaliza kudya, wadachita chimchijha wadatenga chikho chija ni kukamba, "Divai iyi ili mchikho ni chipangano cha chipano icho chichitidwa kwa mwazi wanga, uwo umwazika ndande yanu."