Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 17

20 Yesu wadaayangha, "Ndande ya chikhulupi chanu chochepa. Nikukambilani uzene, ngati mdakakhala ni chikulupi ngati mbeu ya aladali, mdakakhoza kulikambila phili ili, Chokapo upite yaponalo udakapita. Palibe chindhu icho sichilepeleke kwanu.

Veja também