18 Yesu wadajha pafupi pao ni kwaakambila, "Napachidwa ulamulilo wa kuchogoza kumwamba ni jhiko lapanjhi. 19 Chipano pitani kwa wandhu maiko yonjhe, mkaachite kukhala oyaluzidwa, mkaabatize kwa jhina la Atate ni la Mwana ni la Mzimu Woyela,
Publicidade