Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 28

2 Kwa chizulumukila, kudali chimtingiza chachikulu, mtumiki wa kumwamba wa Amnungu wadachika kuchokela kumwamba adapita kuchiliza ni kuugadabula mwala ujha ni kuukhalila. 3 Mtumiki wa kumwamba yujha wamang’azikila ngati mbhambe, ni njhalu zake zidali zoyela mbee. 4 Alonda wajha adaopa kupunda, amatendhemela ni adaoneka ngati amwalila.

Veja também